Deuteronomo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+ 2 Mafumu 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Elisa anauza mayi amene anamuukitsira mwana uja,+ kuti: “Nyamuka, iwe ndi banja lako, ukakhale monga mlendo kulikonse kumene ungakakhale,+ chifukwa Yehova abweretsa njala.+ Njalayo idzatenga zaka 7.”+ Ezekieli 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iwe mwana wa munthu, ngati dziko landichimwira pochita zosakhulupirika,+ ndidzalitambasulira dzanja langa n’kuthyola ndodo zake zimene amakolowekapo mikate yoboola pakati.+ Komanso ndidzalitumizira njala+ ndipo ndidzapha anthu ndi ziweto m’dzikolo.”+
23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+
8 Tsopano Elisa anauza mayi amene anamuukitsira mwana uja,+ kuti: “Nyamuka, iwe ndi banja lako, ukakhale monga mlendo kulikonse kumene ungakakhale,+ chifukwa Yehova abweretsa njala.+ Njalayo idzatenga zaka 7.”+
13 “Iwe mwana wa munthu, ngati dziko landichimwira pochita zosakhulupirika,+ ndidzalitambasulira dzanja langa n’kuthyola ndodo zake zimene amakolowekapo mikate yoboola pakati.+ Komanso ndidzalitumizira njala+ ndipo ndidzapha anthu ndi ziweto m’dzikolo.”+