Genesis 41:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ng’ombe 7 zowonda ndi zonyansazo, zimene zinatuluka pambuyo pa zoyamba zija, zikuimira zaka 7. Koma ngala 7 zimenezo, zopanda kanthu ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa,+ zidzakhala zaka 7 za njala.+ 2 Samueli 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Gadi anapita kwa Davide ndi kumuuza kuti:+ “Kodi m’dziko lanu mubwere njala yaikulu zaka 7,+ kapena muzithawa adani anu akukuthamangitsani miyezi itatu,+ kapena kodi kugwe mliri wa masiku atatu m’dziko lanu?+ Ganizirani mofatsa zoti ndikayankhe kwa Amene wandituma.” Amosi 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+
27 Ng’ombe 7 zowonda ndi zonyansazo, zimene zinatuluka pambuyo pa zoyamba zija, zikuimira zaka 7. Koma ngala 7 zimenezo, zopanda kanthu ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa,+ zidzakhala zaka 7 za njala.+
13 Pamenepo Gadi anapita kwa Davide ndi kumuuza kuti:+ “Kodi m’dziko lanu mubwere njala yaikulu zaka 7,+ kapena muzithawa adani anu akukuthamangitsani miyezi itatu,+ kapena kodi kugwe mliri wa masiku atatu m’dziko lanu?+ Ganizirani mofatsa zoti ndikayankhe kwa Amene wandituma.”
2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+