-
Genesis 41:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ngʼombe 7 zowonda ndi zonyansazo, zimene zinatuluka pambuyo pa zoyamba zija, zikuimira zaka 7. Komanso ngala 7 zopanda kanthu ndiponso zowauka ndi mphepo yakumʼmawa, zidzakhala zaka 7 za njala.
-