Genesis 41:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ng’ombe 7 zowonda ndi zonyansazo, zimene zinatuluka pambuyo pa zoyamba zija, zikuimira zaka 7. Koma ngala 7 zimenezo, zopanda kanthu ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa,+ zidzakhala zaka 7 za njala.+
27 Ng’ombe 7 zowonda ndi zonyansazo, zimene zinatuluka pambuyo pa zoyamba zija, zikuimira zaka 7. Koma ngala 7 zimenezo, zopanda kanthu ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa,+ zidzakhala zaka 7 za njala.+