2 Mafumu 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anayambanso kuyenda uku ndi uku m’nyumbamo. Atatero anapitanso kukaweramira mwanayo. Pamenepo mwanayo anayamba kuyetsemula mpaka maulendo 7, kenako anapenya.+
35 Anayambanso kuyenda uku ndi uku m’nyumbamo. Atatero anapitanso kukaweramira mwanayo. Pamenepo mwanayo anayamba kuyetsemula mpaka maulendo 7, kenako anapenya.+