-
2 Mafumu 8:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Gehazi akufotokozera mfumuyo mmene Elisa anaukitsira munthu wakufa,+ anangomva mayi wa mwana amene anaukitsidwayo akudandaulira mfumu kuti imupatse nyumba yake ndi munda wake.+ Nthawi yomweyo Gehazi anati: “Mbuye wanga+ mfumu, mayiyo ndi uyu, ndiponso mwana wake amene Elisa anamuukitsa uja ndi uyu.”
-