Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndidzathyola kunyada kwanuko, ndi kuchititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati mkuwa.

  • Deuteronomo 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+

  • 1 Mafumu 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 “Kumwamba kukatsekeka, mvula n’kumakanika kugwa+ chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno iwo n’kupemphera atayang’ana malo ano,+ ndi kutamanda dzina lanu ndiponso kusiya tchimo lawo chifukwa choti mwakhala mukuwasautsa,+

  • 1 Mafumu 17:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Eliya+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi+ analankhula ndi Ahabu kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli+ amene ndimam’tumikira,+ sikugwa mame kapena mvula+ zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditalamula.”+

  • Yeremiya 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Alimi achita manyazi moti aphimba mitu yawo chifukwa chakuti m’dzikomo simunagwe mvula+ ndipo nthaka yawonongeka.+

  • Amosi 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Ine ndinakumanani mvula kutatsala miyezi itatu kuti mukolole.+ Ndinagwetsa mvula pamzinda umodzi koma pamzinda wina sindinagwetsepo mvula. Mvula inagwa pamunda umodzi koma pamunda wina sindinagwetsepo mvula ndipo unauma.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena