Deuteronomo 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+ 1 Mafumu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Eliya+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi+ analankhula ndi Ahabu kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli+ amene ndimam’tumikira,+ sikugwa mame kapena mvula+ zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditalamula.”+
17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+
17 Eliya+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi+ analankhula ndi Ahabu kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli+ amene ndimam’tumikira,+ sikugwa mame kapena mvula+ zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditalamula.”+