Deuteronomo 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+ Luka 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Poyankha mngeloyo anamuuza kuti: “Ine ndine Gabirieli,+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu, ndipo wandituma kudzalankhula+ nawe ndi kudzalengeza uthenga wabwino wa zinthu izi kwa iwe.
8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+
19 Poyankha mngeloyo anamuuza kuti: “Ine ndine Gabirieli,+ amene ndimaima pamaso pa Mulungu, ndipo wandituma kudzalankhula+ nawe ndi kudzalengeza uthenga wabwino wa zinthu izi kwa iwe.