Danieli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ndinamva mawu a munthu wochokera kufumbi ali pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anafuula kuti: “Gabirieli,+ thandiza uyo ali apoyo kuti amvetsetse zimene waona.”+ Danieli 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 inde, pamene ndinali kulankhula zimenezi m’pemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona m’masomphenya nditatopa kwambiri poyamba paja,+ ndinamuona akubwera kwa ine pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo, yoperekedwa ngati mphatso.+ Aheberi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+
16 Kenako ndinamva mawu a munthu wochokera kufumbi ali pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anafuula kuti: “Gabirieli,+ thandiza uyo ali apoyo kuti amvetsetse zimene waona.”+
21 inde, pamene ndinali kulankhula zimenezi m’pemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona m’masomphenya nditatopa kwambiri poyamba paja,+ ndinamuona akubwera kwa ine pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo, yoperekedwa ngati mphatso.+
14 Kodi angelo onse si mizimu+ yotumikira ena,+ yotumidwa kukatumikira amene adzalandire chipulumutso monga cholowa chawo?+