Danieli 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 inde, ndili mkati molankhula zimenezi mʼpemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona mʼmasomphenya poyamba paja,+ anabwera kwa ine nditatopa kwambiri, pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo imene imaperekedwa ngati mphatso. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:21 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 184-185
21 inde, ndili mkati molankhula zimenezi mʼpemphero, munthu uja Gabirieli,+ amene ndinamuona mʼmasomphenya poyamba paja,+ anabwera kwa ine nditatopa kwambiri, pa nthawi yopereka nsembe yamadzulo imene imaperekedwa ngati mphatso.