Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi pakati pa mafano opanda pake a mitundu ya anthu pali fano lililonse+ limene lingagwetse mvula? Kapena kodi kumwamba pakokha kungagwetse mvula yamvumbi?+ Kodi si inu Yehova Mulungu wathu+ amene mumachititsa zimenezi? Chiyembekezo chathu chili mwa inu chifukwa ndinu amene mumachititsa zonsezi.+

  • Luka 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mwachitsanzo, ndikukuuzani ndithu kuti, Munali akazi ambiri amasiye mu Isiraeli m’masiku a Eliya, pamene kumwamba kunatsekedwa zaka zitatu ndi miyezi 6, mwakuti m’dziko lonse munagwa njala yaikulu.+

  • Yakobo 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Eliya anali munthu monga ife tomwe,+ komabe anapemphera kuti mvula isagwe,+ ndipo mvula sinagwe kumeneko kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena