Salimo 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+ Salimo 130:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndayembekezera thandizo lanu, inu Yehova. Moyo wanga wayembekezera thandizo lanu.+Ine ndayembekezera mawu anu.+
3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+
5 Ndayembekezera thandizo lanu, inu Yehova. Moyo wanga wayembekezera thandizo lanu.+Ine ndayembekezera mawu anu.+