Levitiko 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+ Deuteronomo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+
21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+
23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+