Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+

  • 1 Mafumu 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 “Kumwamba kukatsekeka, mvula n’kumakanika kugwa+ chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno iwo n’kupemphera atayang’ana malo ano,+ ndi kutamanda dzina lanu ndiponso kusiya tchimo lawo chifukwa choti mwakhala mukuwasautsa,+

  • 2 Mbiri 7:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndikatseka kumwamba kuti mvula isagwe,+ ndikalamula dzombe kuti lidye zomera za m’dzikoli,+ ndikatumiza mliri pakati pa anthu anga,+

  • Yesaya 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndidzangousiya kuti uwonongeke.+ Sindidzatengulira mitengo yake ndipo sindidzaulimanso.+ M’mundamo mudzamera tchire ndi zitsamba zaminga,+ ndipo ndidzalamula mitambo kuti isagwetsere mvula pamundawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena