Oweruza 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kulikonse kumene apita, dzanja la Yehova linali kuwaukira ndi kuwadzetsera masoka,+ monga mmene Yehova ananenera ndiponso monga mmene Yehova analumbirira kwa iwo,+ moti iwo anali kuvutika kwambiri.+ Yesaya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthuwo sanabwerere kwa amene akuwamenya+ ndipo sanafunefune Yehova wa makamu,+ Ezekieli 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Chotero ine ndidzaweruza aliyense wa inu malinga ndi njira zake,+ inu a nyumba ya Isiraeli,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Lapani ndi kusiya zolakwa zanu zonse+ ndipo musalole kuti chilichonse chizikupunthwitsani ndi kukulakwitsani.+
15 Kulikonse kumene apita, dzanja la Yehova linali kuwaukira ndi kuwadzetsera masoka,+ monga mmene Yehova ananenera ndiponso monga mmene Yehova analumbirira kwa iwo,+ moti iwo anali kuvutika kwambiri.+
30 “‘Chotero ine ndidzaweruza aliyense wa inu malinga ndi njira zake,+ inu a nyumba ya Isiraeli,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Lapani ndi kusiya zolakwa zanu zonse+ ndipo musalole kuti chilichonse chizikupunthwitsani ndi kukulakwitsani.+