Deuteronomo 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ukakakhala ndi ana ndi zidzukulu ndipo mwakhala nthawi yaitali m’dzikomo, n’kuchita zinthu zokuwonongetsa+ mwa kupanga chifaniziro,+ chifaniziro cha chinthu chilichonse, n’kuchita choipa pamaso pa Yehova Mulungu wako,+ moti n’kumulakwira, Deuteronomo 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+ Deuteronomo 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti adzapatutsa ana ako aamuna kuti asanditsatire ndipo adzatumikira ndithu milungu ina.+ Pamenepo mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani ndipo adzakuwonongani ndithu mofulumira.+
25 “Ukakakhala ndi ana ndi zidzukulu ndipo mwakhala nthawi yaitali m’dzikomo, n’kuchita zinthu zokuwonongetsa+ mwa kupanga chifaniziro,+ chifaniziro cha chinthu chilichonse, n’kuchita choipa pamaso pa Yehova Mulungu wako,+ moti n’kumulakwira,
26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+
4 Pakuti adzapatutsa ana ako aamuna kuti asanditsatire ndipo adzatumikira ndithu milungu ina.+ Pamenepo mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani ndipo adzakuwonongani ndithu mofulumira.+