Ekisodo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Pita, tsika, chifukwa anthu ako amene unawatsogolera potuluka m’dziko la Iguputo achita zinthu zowawonongetsa.+ Deuteronomo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Musamale kuti musachite zinthu zokuwonongetsani,+ kutinso musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse, chachimuna kapena chachikazi,+
7 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Pita, tsika, chifukwa anthu ako amene unawatsogolera potuluka m’dziko la Iguputo achita zinthu zowawonongetsa.+
16 Musamale kuti musachite zinthu zokuwonongetsani,+ kutinso musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse, chachimuna kapena chachikazi,+