Ekisodo 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako mudzatenga ena mwa ana awo aakazi kuti akhale akazi a ana anu aamuna,+ ndipo ana awo aakazi adzachita chiwerewere ndi milungu yawo, n’kuchititsa ana anu aamuna kuchita chiwerewere ndi milungu yawo.+ 1 Mafumu 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake.
16 Kenako mudzatenga ena mwa ana awo aakazi kuti akhale akazi a ana anu aamuna,+ ndipo ana awo aakazi adzachita chiwerewere ndi milungu yawo, n’kuchititsa ana anu aamuna kuchita chiwerewere ndi milungu yawo.+
4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake.