Deuteronomo 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+ Oweruza 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ana a Amoni anali kuwoloka Yorodano kukamenyana ndi fuko la Yuda, la Benjamini, ndi la Efuraimu, moti Isiraeli anasautsika kwambiri.+
30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+
9 Ndipo ana a Amoni anali kuwoloka Yorodano kukamenyana ndi fuko la Yuda, la Benjamini, ndi la Efuraimu, moti Isiraeli anasautsika kwambiri.+