Deuteronomo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+ 2 Mbiri 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthuwo anagonjetsana chifukwa anaukirana okhaokha. Fuko limodzi linkamenyana ndi fuko lina+ ndiponso mzinda ndi mzinda wina, popeza Mulungu anawasiya pa chisokonezo ndi zowawa zosiyanasiyana.+
25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+
6 Anthuwo anagonjetsana chifukwa anaukirana okhaokha. Fuko limodzi linkamenyana ndi fuko lina+ ndiponso mzinda ndi mzinda wina, popeza Mulungu anawasiya pa chisokonezo ndi zowawa zosiyanasiyana.+