Oweruza 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kulikonse kumene ankapita, dzanja la Yehova linkawaukira ndi kuwabweretsera tsoka,+ mogwirizana ndi zimene Yehova ananena ndiponso zimene Yehova anawalumbirira,+ moti iwo ankavutika kwambiri.+
15 Kulikonse kumene ankapita, dzanja la Yehova linkawaukira ndi kuwabweretsera tsoka,+ mogwirizana ndi zimene Yehova ananena ndiponso zimene Yehova anawalumbirira,+ moti iwo ankavutika kwambiri.+