Oweruza 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kulikonse kumene apita, dzanja la Yehova linali kuwaukira ndi kuwadzetsera masoka,+ monga mmene Yehova ananenera ndiponso monga mmene Yehova analumbirira kwa iwo,+ moti iwo anali kuvutika kwambiri.+
15 Kulikonse kumene apita, dzanja la Yehova linali kuwaukira ndi kuwadzetsera masoka,+ monga mmene Yehova ananenera ndiponso monga mmene Yehova analumbirira kwa iwo,+ moti iwo anali kuvutika kwambiri.+