Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+ Yeremiya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘“Mzinda uwu ndaukana* ndipo ukumana ndi tsoka osati zabwino,”+ watero Yehova. “Ndidzaupereka m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha ndi moto.”+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
10 “‘“Mzinda uwu ndaukana* ndipo ukumana ndi tsoka osati zabwino,”+ watero Yehova. “Ndidzaupereka m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha ndi moto.”+