Yeremiya 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova wanena kuti, ‘Mzinda uno udzaperekedwa ndithu m’manja mwa gulu lankhondo la mfumu ya Babulo, ndipo mfumuyo idzaulanda ndithu.’”+
3 Yehova wanena kuti, ‘Mzinda uno udzaperekedwa ndithu m’manja mwa gulu lankhondo la mfumu ya Babulo, ndipo mfumuyo idzaulanda ndithu.’”+