Deuteronomo 28:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Udzapita ndi mbewu zambiri kumunda, koma udzakolola zochepa+ chifukwa dzombe lidzadya mbewuzo.+