Yesaya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti maekala 10*+ a munda wa mpesa adzatulutsa mtsuko*+ umodzi wokha wa vinyo, ndipo mbewu zokwana muyezo umodzi wa homeri* zidzatulutsa zokolola zokwana muyezo umodzi wokha wa efa.*+ Hagai 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwafesa mbewu zambiri koma zokolola zanu n’zochepa.+ Mukudya koma simukukhuta.+ Mukumwa koma simukukhutira.* Mukuvala zovala koma simukumva kutentha. Amene akugwira ganyu akulandirira ndalama zake m’matumba obowoka.’”+
10 Pakuti maekala 10*+ a munda wa mpesa adzatulutsa mtsuko*+ umodzi wokha wa vinyo, ndipo mbewu zokwana muyezo umodzi wa homeri* zidzatulutsa zokolola zokwana muyezo umodzi wokha wa efa.*+
6 Mwafesa mbewu zambiri koma zokolola zanu n’zochepa.+ Mukudya koma simukukhuta.+ Mukumwa koma simukukhutira.* Mukuvala zovala koma simukumva kutentha. Amene akugwira ganyu akulandirira ndalama zake m’matumba obowoka.’”+