Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 “M’dzikomo mukagwa njala,+ mliri,+ mphepo yotentha yowononga mbewu, matenda ambewu a chuku,+ dzombe,+ mphemvu,+ komanso adani awo akawaukira m’zipata za mizinda yawo, ndiponso kukagwa mliri wamtundu uliwonse, nthenda yamtundu uliwonse,

  • 2 Mbiri 6:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “M’dzikomo mukagwa njala,+ mliri,+ mphepo yotentha yowononga mbewu,+ matenda a mbewu a chuku,+ dzombe,+ mphemvu,+ komanso adani+ awo akawaukira m’zipata za mizinda yawo,+ ndiponso kukagwa mliri wamtundu wina uliwonse, nthenda yamtundu wina uliwonse,+

  • Yoweli 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Patsogolo pawo moto wawononga+ ndipo kumbuyo kwawo moto walawilawi ukunyeketsa.+ Patsogolo pawo pali dziko ngati la Edeni+ koma kumbuyo kwawo kuli chipululu chowonongeka ndipo palibe chilichonse chopulumuka.

  • Yoweli 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndidzakubwezerani mbewu za zaka zonse zimene dzombe ndi ana a dzombe oyenda pansi opanda mapiko, mphemvu ndi mbozi zinadya. Limeneli ndi gulu langa lankhondo lamphamvu limene ndinatumiza pakati panu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena