Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Tsopano zinachitika kuti, m’masiku amene oweruza+ anali atsogoleri, m’dzikomo munagwa njala.+ Ndiyeno munthu wina anasamuka ku Betelehemu+ wa ku Yuda kukakhala m’dziko la Mowabu+ monga mlendo. Anasamuka ndi mkazi wake ndi ana ake awiri aamuna.

  • 2 Mafumu 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Patapita nthawi, mu Samariya+ munagwa njala yaikulu. Asiriyawo anapitirizabe kuzungulira mzindawo mpaka mtengo wogulira mutu wa bulu+ unafika pa ndalama 80 zasiliva, ndipo zitosi za nkhunda+ zodzaza manja awiri* mtengo wake unafika pa ndalama zisanu zasiliva.

  • 2 Mbiri 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 ‘Likatigwera tsoka,+ lupanga, chiweruzo chowawa, mliri+ kapena njala,+ tiziima pamaso pa nyumba iyi+ ndi pamaso panu (popeza dzina lanu+ lili m’nyumba iyi), kuti tifuulire inu kuti mutithandize m’masautso athu, ndipo inu muzimva ndi kutipulumutsa.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena