Levitiko 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndikadzathyola ndodo zanu zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi, ndipo adzakugawirani mochita kukuyezerani pamuyezo.+ Chotero mudzadya koma simudzakhuta.+ Deuteronomo 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Lidzakhala lotembereredwa dengu lako+ ndi chiwiya chako chokandiramo ufa.+ 2 Mafumu 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tikati, ‘Tiyeni tilowe mumzinda,’ tikafera momwemo chifukwa muli njala.+ Tikatinso tikhale pano, tifa. Ndiye tiyeni tikalowe mumsasa wa Asiriya. Akakatisiya ndi moyo, tikhala ndi moyo, koma akakatipha, chabwino tikafa.”+ Maliro 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene anaphedwa ndi lupanga+ aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala,+Pakuti amene anafa ndi njala anafooka chifukwa chosowa chakudya, ndipo anakhala ngati apyozedwa ndi lupanga.
26 Ndikadzathyola ndodo zanu zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi, ndipo adzakugawirani mochita kukuyezerani pamuyezo.+ Chotero mudzadya koma simudzakhuta.+
4 Tikati, ‘Tiyeni tilowe mumzinda,’ tikafera momwemo chifukwa muli njala.+ Tikatinso tikhale pano, tifa. Ndiye tiyeni tikalowe mumsasa wa Asiriya. Akakatisiya ndi moyo, tikhala ndi moyo, koma akakatipha, chabwino tikafa.”+
9 Amene anaphedwa ndi lupanga+ aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala,+Pakuti amene anafa ndi njala anafooka chifukwa chosowa chakudya, ndipo anakhala ngati apyozedwa ndi lupanga.