Yeremiya 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wanena kuti, ‘Amene adzapitirize kukhala mumzinda uno adzafa ndi lupanga,+ njala yaikulu+ kapena mliri.+ Koma amene adzadzipereke kwa Akasidi adzakhala ndi moyo. Adzapulumutsa moyo wake, sadzafa ayi.’+
2 “Yehova wanena kuti, ‘Amene adzapitirize kukhala mumzinda uno adzafa ndi lupanga,+ njala yaikulu+ kapena mliri.+ Koma amene adzadzipereke kwa Akasidi adzakhala ndi moyo. Adzapulumutsa moyo wake, sadzafa ayi.’+