-
Yeremiya 29:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 “‘Ndidzawathamangitsa ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri, ndipo ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho.+ Ndidzawachititsa kukhala chinthu chotembereredwa, chodabwitsa, chochilizira mluzu ndiponso chotonzedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu a kumene ndidzawabalalitsirako.+
-