Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kunja lupanga lidzawasandutsa anamfedwa,+

      Ndipo mkati mwa nyumba, mantha adzawasandutsa anamfedwa.+

      Zimenezi zidzawaphera anyamata ndi anamwali,+

      Mwana woyamwa pamodzi ndi munthu wa imvi.+

  • Yeremiya 21:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Anthu amene adzakhalabe mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.+ Koma amene adzatuluka ndi kugwidwa ndi Akasidi amene akuzungulirani adzakhala ndi moyo. Iwo adzapulumutsa moyo wawo.”’+

  • Yeremiya 27:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kodi iweyo ndi anthu ako muferenji ndi lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri?+ Izi ndi zimene Yehova wanena kuti zidzachitikira mtundu umene sukutumikira mfumu ya Babulo.

  • Maliro 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Taonani, inu Yehova. Inetu zandivuta. M’mimba mwanga mukubwadamuka.+

      Mtima wanga wasweka,+ pakuti ndapanduka kwambiri.+

      Panja, lupanga lapha+ ana. M’nyumba, anthu akufanso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena