13 Kodi iweyo ndi anthu ako muferenji ndi lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri?+ Izi ndi zimene Yehova wanena kuti zidzachitikira mtundu umene sukutumikira mfumu ya Babulo.
15 Lupanga+ lili panja ndipo mliri ndi njala zili mkati.+ Yemwe ali kutchire adzaphedwa ndi lupanga, ndipo amene ali mumzinda njala ndi mliri zidzawasakaza.+