Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndidzabweretsa lupanga pa inu lobwezera chilango+ chifukwa cha pangano.+ Pamenepo mudzathawira m’mizinda yanu, ndipo ndidzakutumizirani mliri pakati panu+ ndi kukuperekani m’manja mwa mdani.+

  • 2 Mbiri 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’chaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu,+ Sisaki+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzaukira Yerusalemu (chifukwa iwo anachita zosakhulupirika kwa Yehova).+

  • 2 Mbiri 32:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Pambuyo pa zimenezi ndiponso pambuyo pa ntchito zokhulupirika+ za Hezekiya, Senakeribu+ mfumu ya Asuri+ anabwera n’kudzazungulira Yuda ndipo anamanga misasa pafupi ndi mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Iye anali kuganiza zogonjetsa mizindayo kuti ikhale yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena