1 Mafumu 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero Solomo anayamba kufunafuna kupha Yerobowamu.+ Choncho Yerobowamu ananyamuka n’kuthawira+ ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo. Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira. 1 Mafumu 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno m’chaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu, Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu.
40 Chotero Solomo anayamba kufunafuna kupha Yerobowamu.+ Choncho Yerobowamu ananyamuka n’kuthawira+ ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo. Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira.