1 Mafumu 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno m’chaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu, Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu. 2 Mbiri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’chaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu,+ Sisaki+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzaukira Yerusalemu (chifukwa iwo anachita zosakhulupirika kwa Yehova).+
2 M’chaka chachisanu cha Mfumu Rehobowamu,+ Sisaki+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzaukira Yerusalemu (chifukwa iwo anachita zosakhulupirika kwa Yehova).+