Yoweli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzakubwezerani mbewu za zaka zonseZimene dzombe, ana a dzombe opanda mapiko komanso dzombe losakaza zinadya.Limeneli ndi gulu langa lankhondo limene ndinakutumizirani.+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2020, tsa. 3
25 Ndidzakubwezerani mbewu za zaka zonseZimene dzombe, ana a dzombe opanda mapiko komanso dzombe losakaza zinadya.Limeneli ndi gulu langa lankhondo limene ndinakutumizirani.+