Levitiko 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzathyola kunyada kwanuko, ndi kuchititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati mkuwa. Deuteronomo 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+ Deuteronomo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+
19 Ndidzathyola kunyada kwanuko, ndi kuchititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati mkuwa.
17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani. Adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ ndipo nthaka sidzatulutsa zipatso zake. Pamenepo mudzafafanizika mwamsanga m’dziko labwinolo limene Yehova akukupatsani.+
23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+