Salimo 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi yatsoka sadzachita manyazi,+Ndipo pa nthawi ya njala adzakhuta.+ Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+
25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+