Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 18:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kodi mbuye wanga simunamve zimene ndinachita pamene Yezebeli anapha aneneri a Yehova? Ndinabisa aneneri 100 a Yehova m’phanga.+ Ndinawagawa m’magulu awiri a aneneri 50 gulu lililonse, ndipo ndinali kuwapatsa mkate ndi madzi.+

  • 1 Mafumu 20:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Munthu wina wochokera pakati pa ana a aneneri,*+ pomvera mawu+ a Yehova anauza mnzake kuti: “Ndimenye!” Koma mnzakeyo anakana kum’menya.

  • 2 Mafumu 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mayi wina yemwe anali mmodzi wa akazi a ana+ a aneneri, anafika kwa Elisa n’kulankhula mokweza kuti: “Mtumiki wanu yemwe anali mwamuna wanga anamwalira. Inu mukudziwa bwino kuti mtumiki wanuyo anali woopa+ Yehova. Tsopano kwabwera wangongole+ kudzatenga ana anga onse awiri kuti akakhale akapolo ake.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena