2 Mafumu 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ana a aneneri+ amene anali ku Beteli anabwera kwa Elisa n’kumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?”+ Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa bwino zimenezo.+ Khalani chete.” Amosi 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Amosi anayankha Amaziya kuti: “Ine sindinali mneneri kapena mwana wa mneneri,+ koma ndinali m’busa+ ndiponso woboola nkhuyu.
3 Ndiyeno ana a aneneri+ amene anali ku Beteli anabwera kwa Elisa n’kumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?”+ Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa bwino zimenezo.+ Khalani chete.”
14 Pamenepo Amosi anayankha Amaziya kuti: “Ine sindinali mneneri kapena mwana wa mneneri,+ koma ndinali m’busa+ ndiponso woboola nkhuyu.