1 Mafumu 20:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wina wochokera pakati pa ana a aneneri,*+ pomvera mawu+ a Yehova anauza mnzake kuti: “Ndimenye!” Koma mnzakeyo anakana kum’menya. 2 Mafumu 4:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pambuyo pake, Elisa anabwerera ku Giligala,+ ndipo m’dzikolo munali njala.+ Tsopano ana+ a aneneri anakhala pamaso pake.+ Patapita nthawi, iye anauza mtumiki wake kuti:+ “Teleka mphika waukulu kuti uwaphikire chakudya ana a aneneriwa.”+
35 Munthu wina wochokera pakati pa ana a aneneri,*+ pomvera mawu+ a Yehova anauza mnzake kuti: “Ndimenye!” Koma mnzakeyo anakana kum’menya.
38 Pambuyo pake, Elisa anabwerera ku Giligala,+ ndipo m’dzikolo munali njala.+ Tsopano ana+ a aneneri anakhala pamaso pake.+ Patapita nthawi, iye anauza mtumiki wake kuti:+ “Teleka mphika waukulu kuti uwaphikire chakudya ana a aneneriwa.”+