2 Mafumu 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ana a aneneri+ amene anali ku Beteli anabwera kwa Elisa n’kumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?”+ Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa bwino zimenezo.+ Khalani chete.” 2 Mafumu 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ana a aneneri amene anali ku Yeriko anapita kwa Elisa n’kumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?” Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa bwino zimenezo. Khalani chete.”+ 2 Mafumu 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mneneri Elisa anaitana mmodzi wa ana+ a aneneri n’kumuuza kuti: “Konzeka,*+ nyamula botolo ladothi+ la mafutali m’manja mwako, upite ku Ramoti-giliyadi.+
3 Ndiyeno ana a aneneri+ amene anali ku Beteli anabwera kwa Elisa n’kumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?”+ Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa bwino zimenezo.+ Khalani chete.”
5 Kenako ana a aneneri amene anali ku Yeriko anapita kwa Elisa n’kumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?” Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa bwino zimenezo. Khalani chete.”+
9 Mneneri Elisa anaitana mmodzi wa ana+ a aneneri n’kumuuza kuti: “Konzeka,*+ nyamula botolo ladothi+ la mafutali m’manja mwako, upite ku Ramoti-giliyadi.+