29 Nthawi yomweyo Elisa anauza Gehazi+ kuti: “Kokera chovala chako m’chiuno ndipo uchimange.+ Tenga ndodo yangayi+ uzipita. Ukakumana ndi munthu aliyense panjira usamupatse moni,+ ndipo munthu akakupatsa moni, usamuyankhe. Ukaike ndodo yangayi pankhope ya mwanayo.”+