1 Samueli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mbuye wathu, chonde, lamulani kuti atumiki anu amene ali pamaso panu akufunireni katswiri+ woimba zeze.+ Ndiyeno mzimu woipa wa Mulungu ukabwera pa inu, iye azikuimbirani zezeyo, ndipo inu muzipeza bwino.” 1 Samueli 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno mzimu woipa wa Mulungu ukafika pa Sauli, Davide anali kutenga zeze ndi kumuimbira. Akatero, Sauli anali kupeza bwino, ndipo mzimu woipawo unali kum’chokera.+
16 Mbuye wathu, chonde, lamulani kuti atumiki anu amene ali pamaso panu akufunireni katswiri+ woimba zeze.+ Ndiyeno mzimu woipa wa Mulungu ukabwera pa inu, iye azikuimbirani zezeyo, ndipo inu muzipeza bwino.”
23 Ndiyeno mzimu woipa wa Mulungu ukafika pa Sauli, Davide anali kutenga zeze ndi kumuimbira. Akatero, Sauli anali kupeza bwino, ndipo mzimu woipawo unali kum’chokera.+