Deuteronomo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Limbani mtima ndipo chitani zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono.”+ Yoswa 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
6 Limbani mtima ndipo chitani zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pang’ono.”+
5 Palibe amene adzatha kulimbana nawe masiku onse a moyo wako.+ Ndidzakhala nawe+ monga mmene ndinakhalira ndi Mose, sindidzakutaya kapena kukusiya ngakhale pang’ono.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+