1 Samueli 14:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 M’masiku onse a Sauli, Afilisiti anali kupanikizidwa ndi nkhondo.+ Ndipo Sauli akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, anali kum’tenga kuti akhale msilikali wake.+ 1 Samueli 17:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mtumiki wanu anapha zonse ziwiri, mkangowo ndi chimbalangondocho. Mfilisiti wosadulidwayu+ akhalanso ngati chimodzi mwa zilombo zimenezi, chifukwa watonza+ asilikali+ a Mulungu wamoyo.”+
52 M’masiku onse a Sauli, Afilisiti anali kupanikizidwa ndi nkhondo.+ Ndipo Sauli akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, anali kum’tenga kuti akhale msilikali wake.+
36 Mtumiki wanu anapha zonse ziwiri, mkangowo ndi chimbalangondocho. Mfilisiti wosadulidwayu+ akhalanso ngati chimodzi mwa zilombo zimenezi, chifukwa watonza+ asilikali+ a Mulungu wamoyo.”+