Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Choncho Davide anadzuka m’mawa kwambiri, atasiya nkhosa zake m’manja mwa wozisamalira. Iye ananyamula katundu wake ndi kunyamuka monga mmene Jese, bambo ake, anamuuzira.+ Atafika mkati mwa mpanda wa msasa,+ anapeza asilikali akupita kumalo omenyera nkhondo,+ akufuula mfuwu ya nkhondo.

  • 1 Mbiri 12:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Onsewa anali amuna ankhondo, okhalira limodzi pamzere wa omenya nkhondo. Iwo anapita ndi mtima wathunthu+ ku Heburoni kukalonga Davide kukhala mfumu ya Isiraeli yense. Ndiponso Aisiraeli ena onse otsala anali ndi mtima umodzi wolonga Davide ufumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena