1 Samueli 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afilisitiwo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo+ kuti amenyane ndi Aisiraeli. Nkhondoyo sinawayendere bwino Aisiraeli, moti anagonjetsedwa ndi Afilisiti.+ Iwo anakantha amuna achiisiraeli pafupifupi 4,000 nkhondoyo ili mkati. 1 Samueli 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amuna amene anali kuyenda ndi Davide anamuyankha kuti: “Ngati tikuchita mantha tili mbali ino ya Yuda,+ ndiye kuli bwanji tikapita ku Keila kukamenyana ndi asilikali a Afilisiti!”+
2 Afilisitiwo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo+ kuti amenyane ndi Aisiraeli. Nkhondoyo sinawayendere bwino Aisiraeli, moti anagonjetsedwa ndi Afilisiti.+ Iwo anakantha amuna achiisiraeli pafupifupi 4,000 nkhondoyo ili mkati.
3 Amuna amene anali kuyenda ndi Davide anamuyankha kuti: “Ngati tikuchita mantha tili mbali ino ya Yuda,+ ndiye kuli bwanji tikapita ku Keila kukamenyana ndi asilikali a Afilisiti!”+